Synopsis
Radio Maria Malawi
Episodes
-
-
-
Kalata ya Aepiskopi Achikatolika M'malawi
09/05/2018 Duration: 01h37minKalata ya Aepiskopi Achikatolika M'malawi
-
Nzotheka ndi Ambuye _ Rev. Fr. Peter Mkhwayi
04/10/2017 Duration: 01h14minBambo Peter Mkhwayi anachita ngozi yoopsa ya galimoto pa 01 October 2016 mpaka kuduka mkono wakumanja. Kodi anamva bwanji mmoyo wao atazindikira kuti mkono umodzi waduka. Kodi moyo wao wachikhulupiro unagwedezeka bwanji?
-
Tikuziona Bwanji Zovinavina pa Chipembedzo
29/03/2017 Duration: 01h06minBambo Enock Kanjira kuyankha funso loti TIKUZIONA BWANJI ZOVINAVINA PACHIPEMBEDZO.
-
Ulaliki wa Ulemelero wa Pansi Pano_Bambo Joseph Kimu
29/03/2017 Duration: 01h09minBambo Joseph Kimu ndi Funghai Mutsinze kukambirana za zotsatira za ulaliki umene umalonjeza anthu ulemelero wa pompopompo kapena kuti Gospel of Prosperity.
-
Tiphunzitseni Kupemphera
23/03/2017 Duration: 01h09minPologamu ya padera ndi Bambo Elizeo Nthalika yokhudza buku lomwe alemba lotchedwa Tiphunzitseni Kupemphera.
-
Chikondi Cha Mulungu Chilibe Malire; Sister Agnes Chimbayo
16/03/2017 Duration: 51minSister Agnes Chimbayo omwe amatumikira ku California ku United States of America kuphunzitsa za CHIKONDI CHA MULUNGU CHILIBE MALIRE
-
Pologalamu yapadera ndi Ambuye Montfort Stima Episkopi wa Dayosizi ya Mangochi
12/03/2017 Duration: 01h09minBambo Joseph Kimu akucheza ndi Ambuye Montfort Sitima, Episkopi wa dayosezi ya Mangochi pa kalata imene iwo alembera akhristu a dayosezi yawo pa nyengo ino ya Lenti.
-
Malawians in Dubai
10/03/2017 Duration: 28minAmalawi omwe akugwira ntchito ku United Arab Emirates (UAE) anali ndi msonkhano komanso nkumano ndi kuchita masewera amitundumitundi ndi cholinga cholimbikitsa umodzi wa a Malawi mu liyenda
-